1 Samueli 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aisiraeli amene ankakhala kuchigwa ndiponso mʼdera la Yorodano ataona kuti asilikali a Isiraeli athawa komanso kuti Sauli ndi ana ake afa, anachoka mʼmizinda yawo nʼkuthawa.+ Kenako Afilisiti anabwera kudzakhala mʼmizindayo.
7 Aisiraeli amene ankakhala kuchigwa ndiponso mʼdera la Yorodano ataona kuti asilikali a Isiraeli athawa komanso kuti Sauli ndi ana ake afa, anachoka mʼmizinda yawo nʼkuthawa.+ Kenako Afilisiti anabwera kudzakhala mʼmizindayo.