1 Samueli 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anadula mutu wa Sauli nʼkumuvula zida zake. Kenako anauza anthu mʼdziko lonse la Afilisiti kuti afalitse uthengawu+ mʼnyumba* za mafano awo+ ndiponso kwa anthu awo.
9 Iwo anadula mutu wa Sauli nʼkumuvula zida zake. Kenako anauza anthu mʼdziko lonse la Afilisiti kuti afalitse uthengawu+ mʼnyumba* za mafano awo+ ndiponso kwa anthu awo.