1 Samueli 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atatero, anatenga mafupa awo+ nʼkuwaika mʼmanda pansi pa mtengo wa bwemba ku Yabesi+ ndipo anasala kudya masiku 7.
13 Atatero, anatenga mafupa awo+ nʼkuwaika mʼmanda pansi pa mtengo wa bwemba ku Yabesi+ ndipo anasala kudya masiku 7.