2 Samueli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Sauli atamwalira, ndiponso Davide atabwera kuchokera kokagonjetsa* Aamaleki, Davideyo anakhala ku Zikilaga+ masiku awiri.
1 Sauli atamwalira, ndiponso Davide atabwera kuchokera kokagonjetsa* Aamaleki, Davideyo anakhala ku Zikilaga+ masiku awiri.