2 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri aphedwa. Nayenso Sauli ndi mwana wake Yonatani afa.”+
4 Ndiyeno Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri aphedwa. Nayenso Sauli ndi mwana wake Yonatani afa.”+