2 Samueli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mnyamatayo anayankha kuti: “Zinangochitika kuti ineyo ndinali paphiri la Giliboa,+ ndipo ndinaona Sauli atatsamira mkondo wake. Asilikali oyenda mʼmagaleta ndi asilikali okwera pamahatchi anali atamupeza.+
6 Mnyamatayo anayankha kuti: “Zinangochitika kuti ineyo ndinali paphiri la Giliboa,+ ndipo ndinaona Sauli atatsamira mkondo wake. Asilikali oyenda mʼmagaleta ndi asilikali okwera pamahatchi anali atamupeza.+