2 Samueli 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atatero, anayamba kulira ndi kusala kudya+ mpaka madzulo. Iwo ankalira maliro a Sauli, mwana wake Yonatani, anthu a Yehova ndiponso nyumba ya Isiraeli+ chifukwa anali ataphedwa ndi lupanga.
12 Atatero, anayamba kulira ndi kusala kudya+ mpaka madzulo. Iwo ankalira maliro a Sauli, mwana wake Yonatani, anthu a Yehova ndiponso nyumba ya Isiraeli+ chifukwa anali ataphedwa ndi lupanga.