2 Samueli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anamufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani sunaope kupha wodzozedwa wa Yehova?”+