2 Samueli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Davide anamuuza kuti: “Mlandu wa magazi ako ukhale pamutu pako, chifukwa wadzichitira wekha umboni ponena kuti, ‘Ineyo ndapha wodzozedwa wa Yehova.’”+
16 Davide anamuuza kuti: “Mlandu wa magazi ako ukhale pamutu pako, chifukwa wadzichitira wekha umboni ponena kuti, ‘Ineyo ndapha wodzozedwa wa Yehova.’”+