2 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Isiraeli iwe, anthu ako aulemerero aphedwa pamalo ako okwezeka.+ Anthu amphamvu agwa!