2 Samueli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musanene zimenezi ku Gati;+Musazilengeze mʼmisewu ya Asikeloni,Chifukwa ana aakazi a Afilisiti akhoza kusangalala,Ana aakazi a anthu osadulidwa akhoza kukondwera.
20 Musanene zimenezi ku Gati;+Musazilengeze mʼmisewu ya Asikeloni,Chifukwa ana aakazi a Afilisiti akhoza kusangalala,Ana aakazi a anthu osadulidwa akhoza kukondwera.