2 Samueli 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Uta wa Yonatani sunkalephera kupha adani ndi kukhetsa magazi awo,Sunkalephera kubaya mafuta a anthu amphamvu.+Lupanga la Sauli silinkabwerera osakwaniritsa ntchito yake.+
22 Uta wa Yonatani sunkalephera kupha adani ndi kukhetsa magazi awo,Sunkalephera kubaya mafuta a anthu amphamvu.+Lupanga la Sauli silinkabwerera osakwaniritsa ntchito yake.+