-
2 Samueli 1:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Inu ana aakazi a Isiraeli, mulirireni Sauli,
Amene anakuvekani zovala zamtengo wapatali, zofiira komanso zokhala ndi zokongoletsa,
Amene anaika zokongoletsa zagolide pazovala zanu.
-