2 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Davide anafunsa Yehova kuti:+ “Kodi ndipite mumzinda wina wa Yuda?” Yehova anamuyankha kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+
2 Kenako Davide anafunsa Yehova kuti:+ “Kodi ndipite mumzinda wina wa Yuda?” Yehova anamuyankha kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+