2 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anapitanso ndi amuna amene ankayenda naye,+ aliyense ndi banja lake. Iwo anakakhala mʼmizinda yozungulira Heburoni.
3 Davide anapitanso ndi amuna amene ankayenda naye,+ aliyense ndi banja lake. Iwo anakakhala mʼmizinda yozungulira Heburoni.