2 Samueli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako amuna a ku Yuda anabwera nʼkudzoza Davide kuti akhale mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Iwo anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli mʼmanda.”
4 Kenako amuna a ku Yuda anabwera nʼkudzoza Davide kuti akhale mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Iwo anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli mʼmanda.”