-
2 Samueli 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tsopano limbitsani manja anu ndipo mukhale amuna olimba mtima, chifukwa mbuye wanu Sauli wamwalira ndipo anthu a nyumba ya Yuda andidzoza kuti ndikhale mfumu yawo.”
-