2 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Isi-boseti mwana wa Sauli anali ndi zaka 40 pamene anakhala mfumu ya Isiraeli ndipo analamulira zaka ziwiri. Koma anthu a nyumba ya Yuda ankatsatira Davide.+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2017, tsa. 32
10 Isi-boseti mwana wa Sauli anali ndi zaka 40 pamene anakhala mfumu ya Isiraeli ndipo analamulira zaka ziwiri. Koma anthu a nyumba ya Yuda ankatsatira Davide.+