2 Samueli 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Abineri anauza Yowabu kuti: “Bwanji anyamata athuwa amenyane* tione?” Yowabu anayankha kuti: “Chabwino, amenyanedi.”
14 Kenako Abineri anauza Yowabu kuti: “Bwanji anyamata athuwa amenyane* tione?” Yowabu anayankha kuti: “Chabwino, amenyanedi.”