-
2 Samueli 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako Abineri anauzanso Asaheli kuti: “Siya kundithamangitsa. Ndikuphatu! Ndiye ndikakupha ndidzaonana bwanji ndi mchimwene wako Yowabu?”
-