-
2 Samueli 2:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Zitatero, Yowabu ndi Abisai anayamba kuthamangitsa Abineri. Pamene dzuwa linkalowa, anali atafika paphiri la Ama, limene lili pafupi ndi Giya panjira yopita kuchipululu cha Gibiyoni.
-