-
2 Samueli 2:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Kenako Abineri anafuulira Yowabu kuti: “Kodi tipitiriza kuphana ndi lupanga mpaka liti? Sukudziwa kuti zimenezi zibweretsa mavuto aakulu? Kodi uwauza liti anthuwa kuti asiye kuthamangitsa abale awo?”
-