-
2 Samueli 2:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa ndipo anthu ake anasiya kuthamangitsa Aisiraeli moti nkhondo inathera pomwepo.
-