2 Samueli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo ya pakati pa anthu a nyumba ya Sauli ndi a nyumba ya Davide inapitirirabe. Davide anapitiriza kukhala wamphamvu+ koma anthu a nyumba ya Sauli ankachepa mphamvu.+
3 Nkhondo ya pakati pa anthu a nyumba ya Sauli ndi a nyumba ya Davide inapitirirabe. Davide anapitiriza kukhala wamphamvu+ koma anthu a nyumba ya Sauli ankachepa mphamvu.+