2 Samueli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wake wachiwiri anali Kileyabu ndipo mayi ake anali Abigayeli+ yemwe anali mkazi wa Nabala wa ku Karimeli. Wachitatu anali Abisalomu+ ndipo mayi ake anali Maaka, mwana wa Talimai+ mfumu ya ku Gesuri.
3 Mwana wake wachiwiri anali Kileyabu ndipo mayi ake anali Abigayeli+ yemwe anali mkazi wa Nabala wa ku Karimeli. Wachitatu anali Abisalomu+ ndipo mayi ake anali Maaka, mwana wa Talimai+ mfumu ya ku Gesuri.