2 Samueli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sauli anali ndi mkazi wamngʼono, dzina lake Rizipa,+ mwana wa Aya. Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “Nʼchifukwa chiyani unagona ndi mkazi wamngʼono wa bambo anga?”+
7 Sauli anali ndi mkazi wamngʼono, dzina lake Rizipa,+ mwana wa Aya. Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “Nʼchifukwa chiyani unagona ndi mkazi wamngʼono wa bambo anga?”+