2 Samueli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Davide anayankha kuti: “Chabwino! Ndichitadi nawe pangano. Koma ndikukupempha chinthu chimodzi: Usadzabwere kuno kudzaonana nane pokhapokha udzabwere ndi Mikala,+ mwana wamkazi wa Sauli.”
13 Davide anayankha kuti: “Chabwino! Ndichitadi nawe pangano. Koma ndikukupempha chinthu chimodzi: Usadzabwere kuno kudzaonana nane pokhapokha udzabwere ndi Mikala,+ mwana wamkazi wa Sauli.”