2 Samueli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Davide anatumiza uthenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli wakuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinamuperekera malowolo a makungu okwana 100 a Afilisiti, amene amachotsa pochita mdulidwe.”+
14 Kenako Davide anatumiza uthenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli wakuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinamuperekera malowolo a makungu okwana 100 a Afilisiti, amene amachotsa pochita mdulidwe.”+