2 Samueli 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mwamuna wake ankamutsatira, kwinaku akulira mpaka kukafika ku Bahurimu.+ Kenako Abineri anamuuza kuti: “Bwerera!” Atatero anabwerera.
16 Koma mwamuna wake ankamutsatira, kwinaku akulira mpaka kukafika ku Bahurimu.+ Kenako Abineri anamuuza kuti: “Bwerera!” Atatero anabwerera.