-
2 Samueli 3:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pasanapite nthawi, Yowabu ndi atumiki a Davide anafika kuchokera kunkhondo, atatengako zinthu zambiri. Pa nthawiyi Abineri sanali ndi Davide ku Heburoni chifukwa anali atamulola kupita mwamtendere.
-