-
2 Samueli 3:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndiyeno Yowabu anachoka nʼkumusiya Davide ndipo anatuma anthu kuti akamubweze Abineri. Anthuwo anamupeza Abineri pachitsime cha Sira, koma Davide sanadziwe chilichonse.
-