-
2 Samueli 3:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Kenako Davide anauza Yowabu ndi anthu onse amene anali naye kuti: “Ngʼambani zovala zanu nʼkuvala ziguduli ndipo mumulire Abineri.” Mfumu Davide ankayenda pambuyo pa chithatha cha maliro a Abineri.
-