2 Samueli 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Manja ako anali osamangidwa,Ndipo mapazi ako sanaikidwe mʼmatangadza a kopa. Wafa ngati waphedwa ndi zigawenga.”*+ Zitatero anthu onse analiranso.
34 Manja ako anali osamangidwa,Ndipo mapazi ako sanaikidwe mʼmatangadza a kopa. Wafa ngati waphedwa ndi zigawenga.”*+ Zitatero anthu onse analiranso.