2 Samueli 3:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine lero ndafooka ngakhale kuti ndinadzozedwa kukhala mfumu.+ Ndikuona kuti amuna awa, ana a Zeruya,+ achita nkhanza kwambiri.+ Yehova abwezere munthu aliyense wochita zoipa mogwirizana ndi kuipa kwake.”+
39 Ine lero ndafooka ngakhale kuti ndinadzozedwa kukhala mfumu.+ Ndikuona kuti amuna awa, ana a Zeruya,+ achita nkhanza kwambiri.+ Yehova abwezere munthu aliyense wochita zoipa mogwirizana ndi kuipa kwake.”+