2 Samueli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide ku Heburoni+ nʼkumuuza kuti: “Ife ndi inu ndife magazi amodzi.*+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 17
5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide ku Heburoni+ nʼkumuuza kuti: “Ife ndi inu ndife magazi amodzi.*+