2 Samueli 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kale, pamene Sauli anali mfumu yathu, inuyo ndi amene munkatsogolera Aisiraeli kunkhondo.*+ Ndipo Yehova anakuuzani kuti, ‘Udzaweta anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri wa Aisiraeli.’”+
2 Kale, pamene Sauli anali mfumu yathu, inuyo ndi amene munkatsogolera Aisiraeli kunkhondo.*+ Ndipo Yehova anakuuzani kuti, ‘Udzaweta anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri wa Aisiraeli.’”+