2 Samueli 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Davide analanda malo amene anali mumpanda wolimba kwambiri mu Ziyoni, umene panopa ndi Mzinda wa Davide.+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:7 Mawu a Mulungu, ptsa. 95-96
7 Koma Davide analanda malo amene anali mumpanda wolimba kwambiri mu Ziyoni, umene panopa ndi Mzinda wa Davide.+