-
2 Samueli 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tsiku limenelo, Davide ananena kuti: “Aliyense wokaukira Ayebusi adutse mʼngalande zamadzi nʼkukapha ‘anthu olumala ndi osaona,’ anthu amene ine Davide ndimadana nawo!” Nʼchifukwa chake pali mawu akuti: “Wosaona ndi wolumala sadzalowa mʼnyumba.”
-