2 Samueli 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Davide anayamba kukhala mʼmalo omwe anali mumpanda wolimba kwambiri, ndipo ankadziwika kuti* Mzinda wa Davide. Iye anayamba kumanga malo onsewo kuyambira ku Chimulu cha Dothi*+ mpaka mkati.+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2152
9 Kenako Davide anayamba kukhala mʼmalo omwe anali mumpanda wolimba kwambiri, ndipo ankadziwika kuti* Mzinda wa Davide. Iye anayamba kumanga malo onsewo kuyambira ku Chimulu cha Dothi*+ mpaka mkati.+