2 Samueli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Davide atachoka ku Heburoni nʼkupita ku Yerusalemu anakwatiranso akazi ena komanso anali ndi akazi apambali+ ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.+
13 Davide atachoka ku Heburoni nʼkupita ku Yerusalemu anakwatiranso akazi ena komanso anali ndi akazi apambali+ ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.+