2 Samueli 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Afilisiti atamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli,+ onse anabwera kudzamufunafuna.+ Davide atamva zimenezi, anapita kumalo ovuta kufikako.+
17 Afilisiti atamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli,+ onse anabwera kudzamufunafuna.+ Davide atamva zimenezi, anapita kumalo ovuta kufikako.+