2 Samueli 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Yehova+ kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka mʼmanja mwanga?” Yehova anauza Davide kuti: “Pita, Afilisitiwa ndiwapereka ndithu mʼmanja mwako.”+
19 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Yehova+ kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka mʼmanja mwanga?” Yehova anauza Davide kuti: “Pita, Afilisitiwa ndiwapereka ndithu mʼmanja mwako.”+