2 Samueli 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero anati: “Yehova wayenda patsogolo panga ngati madzi a chigumula nʼkuwononga adani anga.”+ Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Baala-perazimu.*+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:20 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 20-21
20 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero anati: “Yehova wayenda patsogolo panga ngati madzi a chigumula nʼkuwononga adani anga.”+ Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Baala-perazimu.*+