2 Samueli 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi, Afilisiti aja anabweranso nʼkumwazikana mʼchigwa cha Arefai.+