-
2 Samueli 5:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka, ukanyamuke mwamsanga, chifukwa Yehova adzakhala atatsogola kukapha asilikali a Afilisiti.”
-