2 Samueli 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iwo ananyamulira Likasa la Mulungu woona pangolo yatsopano+ kuti alichotse kunyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Uza ndi Ahiyo, ana aamuna a Abinadabu, ndi amene ankatsogolera ngolo yatsopanoyo. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:3 Nsanja ya Olonda,4/1/1996, ptsa. 28-29
3 Koma iwo ananyamulira Likasa la Mulungu woona pangolo yatsopano+ kuti alichotse kunyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Uza ndi Ahiyo, ana aamuna a Abinadabu, ndi amene ankatsogolera ngolo yatsopanoyo.