2 Samueli 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma atafika kumalo opunthira mbewu a ku Nakoni, Uza anagwira Likasa la Mulungu woona,+ chifukwa ngʼombe zinatsala pangʼono kuligwetsa. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 174/1/1996, ptsa. 28-29
6 Koma atafika kumalo opunthira mbewu a ku Nakoni, Uza anagwira Likasa la Mulungu woona,+ chifukwa ngʼombe zinatsala pangʼono kuligwetsa.