2 Samueli 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Uza ndipo Mulungu woona anamuphera+ pomwepo chifukwa chochita zinthu mopanda ulemu.+ Moti Uza anafera pompo, pafupi ndi Likasa la Mulungu woona. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:7 Nsanja ya Olonda,2/1/2005, ptsa. 26-274/1/1996, ptsa. 28-29
7 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Uza ndipo Mulungu woona anamuphera+ pomwepo chifukwa chochita zinthu mopanda ulemu.+ Moti Uza anafera pompo, pafupi ndi Likasa la Mulungu woona.