2 Samueli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Davide anakwiya* chifukwa Yehova anakwiyira kwambiri Uza. Malo amenewa amadziwika ndi dzina lakuti Perezi-uza* mpaka lero. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:8 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 174/1/1996, tsa. 29
8 Koma Davide anakwiya* chifukwa Yehova anakwiyira kwambiri Uza. Malo amenewa amadziwika ndi dzina lakuti Perezi-uza* mpaka lero.