2 Samueli 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho Davide anachita mantha kwambiri ndi Yehova+ tsiku limenelo, ndipo anati: “Kodi Likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:9 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 174/1/1996, tsa. 29
9 Choncho Davide anachita mantha kwambiri ndi Yehova+ tsiku limenelo, ndipo anati: “Kodi Likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+